The Very Best — Nsokoto song lyrics and translation
The page contains the lyrics and English translation of the song "Nsokoto" by The Very Best.
Lyrics
Kumsokoto kuli mfiti imodzi inkalodza ana osalakwa
Kupata kwa ana iyo sinkasangalatsidwa nako
Mwana apate eti tiona ngati agone
Kumsokoto kuli mfiti imodzi inkalodza ana osalakwa
Kupata kwa ana iyo sinkasangalatsidwa nako
Mwana apate eti tiona ngati agone
Chaka chino chokha iye akagonera kumanda
M’mati n’kwere ndakwera panyumba yanthakati
Wakoma bana pawaka
Wamara bana nsokoto
Mwana akangoti agone
Kum’bwerera usiku
Thupi lonse lamangika
Kulephera kufuula
Poti adsuke mam’mawa
Thupi kunjenjemera
Mutu wanga, malungo, matenda aja akula
Wakoma bana
Wati kitasha
Wamara bana
Ichi n’chasoni
Nsokoto nsokoto
Nsokoto nsokoto
Muuze nthakatiyo namulondola ife takana
Bana bakunsokoto ise
Bana bakumulowe ise
Bana bamwakisulu ise
Bana bakaronga ise
Bana bakurumphi ise
Bana bakuchitipa ise
Lyrics translation
Twisting the shipyard the chitch imodzi inkalodza has been divorced
Get to ana sinkasangalatsidwa nako
A son may see a Tiona shirt agone
Twisting the shipyard the chitch imodzi inkalodza has been divorced
Get to ana sinkasangalatsidwa nako
A son may see a Tiona shirt agone
Chaka chino chokha II akagonera kumanda
M n ndakwera mouse sing yanthakati
Lepers pinch catch
Wamara pinch nsokoto
Son akangoti agone
To night
Thupi lonse lamangika
Kindle to follow it
Poti adsuke mam'mawa
Thupi kunjenjemera
Mutu carbohydrates, malungo, act aja akula
Lepers pinch
Kitasha Watts
Mara pinch
Ichi n
Nsokoto nsokoto
Nsokoto nsokoto
Sell nthakatio namulondola to takana
Pinch bakunsokoto ise
Pinch bakumulowe ise
Pinch bamwakisulu ise
Pinch bakaronga ise
Pinch bakurumphi ise
Pinch bakuchitipa ise